Skip to content Skip to sidebar Skip to footer

[DOWNLOAD] "M’mene Mungakwaniritsire Utumiki Wanu" by Dag Heward-Mills " eBook PDF Kindle ePub Free

M’mene Mungakwaniritsire Utumiki Wanu

📘 Read Now     📥 Download


eBook details

  • Title: M’mene Mungakwaniritsire Utumiki Wanu
  • Author : Dag Heward-Mills
  • Release Date : January 25, 2019
  • Genre: Christianity,Books,Religion & Spirituality,
  • Pages : * pages
  • Size : 447 KB

Description

Palibe mwaife amene wayika dongosolo lokafika kumwamba opanda kuchita chomwe Mulungu amafuna kuti ife tikachite padziko lapansi. Ayi, olo ndi mmodzi! Ife tikufuna timalize ntchito Mulungu watipatsa ife. Bukhu ili ndilokhudza mmene mungakwanitsire utumiki wanu. Bukhu ili ndi kalondolondo ka momwe ife tingayankhire zochitika zaumulungu mmoyo mwathu - ndicholinga chosafuna kupezeka operewera patsikulo. Mukakwaniritse utumiki wanu ndipo Mulungu akanene kwa inu, "Wachita bwino, kapolo wabwino ndi okhulupirika!"


PDF Books Download "M’mene Mungakwaniritsire Utumiki Wanu" Online ePub Kindle